Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 14 - فُصِّلَت - Page - Juz 24
﴿إِذۡ جَآءَتۡهُمُ ٱلرُّسُلُ مِنۢ بَيۡنِ أَيۡدِيهِمۡ وَمِنۡ خَلۡفِهِمۡ أَلَّا تَعۡبُدُوٓاْ إِلَّا ٱللَّهَۖ قَالُواْ لَوۡ شَآءَ رَبُّنَا لَأَنزَلَ مَلَٰٓئِكَةٗ فَإِنَّا بِمَآ أُرۡسِلۡتُم بِهِۦ كَٰفِرُونَ ﴾
[فُصِّلَت: 14]
﴿إذ جاءتهم الرسل من بين أيديهم ومن خلفهم ألا تعبدوا إلا الله﴾ [فُصِّلَت: 14]
Khaled Ibrahim Betala “Pamene aneneri adawadzera patsogolo pawo ndi pambuyo pawo (ndikuwauza): “Musapembedze (milungu ina), koma Allah,” adati: “Mbuye wathu akadafuna, akadatsitsa angelo (kudzatilalikira, osati anthu monga inu). Choncho ndithu ife tikuzikana zimene mwatumidwa nazozo.” |