×

Akakhala anthu a Aad, iwo adanyada kopambana padziko ndipo adati, “Kodi ali 41:15 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Fussilat ⮕ (41:15) ayat 15 in Chichewa

41:15 Surah Fussilat ayat 15 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 15 - فُصِّلَت - Page - Juz 24

﴿فَأَمَّا عَادٞ فَٱسۡتَكۡبَرُواْ فِي ٱلۡأَرۡضِ بِغَيۡرِ ٱلۡحَقِّ وَقَالُواْ مَنۡ أَشَدُّ مِنَّا قُوَّةًۖ أَوَلَمۡ يَرَوۡاْ أَنَّ ٱللَّهَ ٱلَّذِي خَلَقَهُمۡ هُوَ أَشَدُّ مِنۡهُمۡ قُوَّةٗۖ وَكَانُواْ بِـَٔايَٰتِنَا يَجۡحَدُونَ ﴾
[فُصِّلَت: 15]

Akakhala anthu a Aad, iwo adanyada kopambana padziko ndipo adati, “Kodi ali ndi mphamvu zopambana zathu ndani?” Kodi iwo saona kuti Mulungu amene adawalenga, ali ndi mphamvu zambiri zoposa zawo? Ndipo iwo anali kukana chivumbulutso chathu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فأما عاد فاستكبروا في الأرض بغير الحق وقالوا من أشد منا قوة, باللغة نيانجا

﴿فأما عاد فاستكبروا في الأرض بغير الحق وقالوا من أشد منا قوة﴾ [فُصِّلَت: 15]

Khaled Ibrahim Betala
“Tsono Âdi adadzikweza pa dziko mosayenera, ndipo adati: “Ndani wamphamvu kuposa ife?” Kodi saona kuti Allah Yemwe adawalenga ndi Mwini mphamvu zambiri kuposa iwo? Koma adapitiriza kukanira zozizwitsa Zathu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek