×

Kotero Ife tidawatumizira mphepo yamkuntho m’masiku a tsoka, ndi cholinga choti alawe 41:16 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Fussilat ⮕ (41:16) ayat 16 in Chichewa

41:16 Surah Fussilat ayat 16 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 16 - فُصِّلَت - Page - Juz 24

﴿فَأَرۡسَلۡنَا عَلَيۡهِمۡ رِيحٗا صَرۡصَرٗا فِيٓ أَيَّامٖ نَّحِسَاتٖ لِّنُذِيقَهُمۡ عَذَابَ ٱلۡخِزۡيِ فِي ٱلۡحَيَوٰةِ ٱلدُّنۡيَاۖ وَلَعَذَابُ ٱلۡأٓخِرَةِ أَخۡزَىٰۖ وَهُمۡ لَا يُنصَرُونَ ﴾
[فُصِّلَت: 16]

Kotero Ife tidawatumizira mphepo yamkuntho m’masiku a tsoka, ndi cholinga choti alawe chilango chochititsa manyazi m’dziko lino koma, ndithudi, chilango cha m’moyo umene uli nkudza ndi chochititsa manyazi zedi ndipo iwo sadzathandizidwa ayi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فأرسلنا عليهم ريحا صرصرا في أيام نحسات لنذيقهم عذاب الخزي في الحياة, باللغة نيانجا

﴿فأرسلنا عليهم ريحا صرصرا في أيام نحسات لنذيقهم عذاب الخزي في الحياة﴾ [فُصِّلَت: 16]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho tidawatumizira mphepo ya mkuntho yozizira kwabasi mmasiku amatsoka, kuti tiwalawitse chilango chowasambula pamoyo wa pa dziko lapansi; ndipo chilango cha tsiku lachimaliziro ndi choyalutsa kwambiri; ndipo iwo sadzapulumutsidwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek