Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 20 - الزُّخرُف - Page - Juz 25
﴿وَقَالُواْ لَوۡ شَآءَ ٱلرَّحۡمَٰنُ مَا عَبَدۡنَٰهُمۗ مَّا لَهُم بِذَٰلِكَ مِنۡ عِلۡمٍۖ إِنۡ هُمۡ إِلَّا يَخۡرُصُونَ ﴾
[الزُّخرُف: 20]
﴿وقالوا لو شاء الرحمن ما عبدناهم ما لهم بذلك من علم إن﴾ [الزُّخرُف: 20]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo (otsutsa) akunena: “Akadafuna (Allah) Wachifundo chambiri (kuti tisamapembedze mafano awa), sitikadawapembedza!” Iwo alibe kudziwa pa zimenezi (zomwe akunenazi). Koma akungonena mawu opeka |