Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 42 - الزُّخرُف - Page - Juz 25
﴿أَوۡ نُرِيَنَّكَ ٱلَّذِي وَعَدۡنَٰهُمۡ فَإِنَّا عَلَيۡهِم مُّقۡتَدِرُونَ ﴾
[الزُّخرُف: 42]
﴿أو نرينك الذي وعدناهم فإنا عليهم مقتدرون﴾ [الزُّخرُف: 42]
Khaled Ibrahim Betala “Kapena tikusonyeza zimene tidawalonjeza (uona ndi maso ako usadafe). Ndithu Ife tili ndi mphamvu pa iwo |