Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 60 - الزُّخرُف - Page - Juz 25
﴿وَلَوۡ نَشَآءُ لَجَعَلۡنَا مِنكُم مَّلَٰٓئِكَةٗ فِي ٱلۡأَرۡضِ يَخۡلُفُونَ ﴾
[الزُّخرُف: 60]
﴿ولو نشاء لجعلنا منكم ملائكة في الأرض يخلفون﴾ [الزُّخرُف: 60]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo tikadafuna tikadawachita angelo kukhala pa dziko mmalo mwa inu ndi kumasiirana iwo kwa iwo (kuti mudziwe kuti angelo akugonjera malamulo a Allah. Iwo siAllah) |