×

Ndipo onse amene amawapembedza oonjezera pa Mulungu alibe mphamvu yowaimirira kupatula yekhayo 43:86 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zukhruf ⮕ (43:86) ayat 86 in Chichewa

43:86 Surah Az-Zukhruf ayat 86 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 86 - الزُّخرُف - Page - Juz 25

﴿وَلَا يَمۡلِكُ ٱلَّذِينَ يَدۡعُونَ مِن دُونِهِ ٱلشَّفَٰعَةَ إِلَّا مَن شَهِدَ بِٱلۡحَقِّ وَهُمۡ يَعۡلَمُونَ ﴾
[الزُّخرُف: 86]

Ndipo onse amene amawapembedza oonjezera pa Mulungu alibe mphamvu yowaimirira kupatula yekhayo amene amachitira umboni woona ndiye amene iwo amamudziwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولا يملك الذين يدعون من دونه الشفاعة إلا من شهد بالحق وهم, باللغة نيانجا

﴿ولا يملك الذين يدعون من دونه الشفاعة إلا من شهد بالحق وهم﴾ [الزُّخرُف: 86]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo omwe akuwapembedzawo kusiya Iye (Allah), sangathe kupulumutsa (aliyense) kupatula amene akuikira umboni choonachi, pomwe iwo akuchidziwa bwino
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek