Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 88 - الزُّخرُف - Page - Juz 25
﴿وَقِيلِهِۦ يَٰرَبِّ إِنَّ هَٰٓؤُلَآءِ قَوۡمٞ لَّا يُؤۡمِنُونَ ﴾
[الزُّخرُف: 88]
﴿وقيله يارب إن هؤلاء قوم لا يؤمنون﴾ [الزُّخرُف: 88]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo zonena zake (Mneneri Muhammad{s.a.w} nthawi zonse): “E Mbuye Wanga! Ndithu awa ndi anthu osakhulupirira (nditani nao)?” |