Quran with Chichewa translation - Surah Ad-Dukhan ayat 41 - الدُّخان - Page - Juz 25
﴿يَوۡمَ لَا يُغۡنِي مَوۡلًى عَن مَّوۡلٗى شَيۡـٔٗا وَلَا هُمۡ يُنصَرُونَ ﴾
[الدُّخان: 41]
﴿يوم لا يغني مولى عن مولى شيئا ولا هم ينصرون﴾ [الدُّخان: 41]
Khaled Ibrahim Betala “Tsiku limene m’bale sadzathandiza m’bale wake pa chilichonse (ku chilango cha Allah), ngakhale iwo sadzapulumutsidwa |