Quran with Chichewa translation - Surah Ad-Dukhan ayat 42 - الدُّخان - Page - Juz 25
﴿إِلَّا مَن رَّحِمَ ٱللَّهُۚ إِنَّهُۥ هُوَ ٱلۡعَزِيزُ ٱلرَّحِيمُ ﴾
[الدُّخان: 42]
﴿إلا من رحم الله إنه هو العزيز الرحيم﴾ [الدُّخان: 42]
Khaled Ibrahim Betala “Kupatula amene Allah adzawachitira chifundo. Ndithu Iye Ngwamphamvu zoposa, Ngwachisoni chosatha |