×

Iwo adati, “Kodi iwe wadza ndi cholinga chotiletsa ife kuti tisapembedze milungu 46:22 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahqaf ⮕ (46:22) ayat 22 in Chichewa

46:22 Surah Al-Ahqaf ayat 22 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahqaf ayat 22 - الأحقَاف - Page - Juz 26

﴿قَالُوٓاْ أَجِئۡتَنَا لِتَأۡفِكَنَا عَنۡ ءَالِهَتِنَا فَأۡتِنَا بِمَا تَعِدُنَآ إِن كُنتَ مِنَ ٱلصَّٰدِقِينَ ﴾
[الأحقَاف: 22]

Iwo adati, “Kodi iwe wadza ndi cholinga chotiletsa ife kuti tisapembedze milungu yathu? Choncho bweretsa kwa ife mavuto amene uli kutiopseza nawo ngati iwe uli kunenadi zoona.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قالوا أجئتنا لتأفكنا عن آلهتنا فأتنا بما تعدنا إن كنت من الصادقين, باللغة نيانجا

﴿قالوا أجئتنا لتأفكنا عن آلهتنا فأتنا بما تعدنا إن كنت من الصادقين﴾ [الأحقَاف: 22]

Khaled Ibrahim Betala
“Adanena: “Ha! Kodi watidzera kuti utipatule ku milungu yathu? Choncho tibweretsere zimene ukutilonjezazo ngati uli mwa onena zoona.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek