Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahqaf ayat 23 - الأحقَاف - Page - Juz 26
﴿قَالَ إِنَّمَا ٱلۡعِلۡمُ عِندَ ٱللَّهِ وَأُبَلِّغُكُم مَّآ أُرۡسِلۡتُ بِهِۦ وَلَٰكِنِّيٓ أَرَىٰكُمۡ قَوۡمٗا تَجۡهَلُونَ ﴾
[الأحقَاف: 23]
﴿قال إنما العلم عند الله وأبلغكم ما أرسلت به ولكني أراكم قوما﴾ [الأحقَاف: 23]
Khaled Ibrahim Betala “Adanena (Hûd): “Ndithu kudziwa (kwenikweni kwa zimenezo) kuli kwa Allah; ndipo ine ndikungofikitsa kwa inu zimene ndatumidwa koma ine ndikukuonani kuti inu ndinu anthu amene mukuchita (zinthu za) umbuli |