×

Kuononga chinthu chilichonse ndi mphamvu ya Ambuye wake. Ndipo pamene kumacha m’mawa 46:25 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahqaf ⮕ (46:25) ayat 25 in Chichewa

46:25 Surah Al-Ahqaf ayat 25 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahqaf ayat 25 - الأحقَاف - Page - Juz 26

﴿تُدَمِّرُ كُلَّ شَيۡءِۭ بِأَمۡرِ رَبِّهَا فَأَصۡبَحُواْ لَا يُرَىٰٓ إِلَّا مَسَٰكِنُهُمۡۚ كَذَٰلِكَ نَجۡزِي ٱلۡقَوۡمَ ٱلۡمُجۡرِمِينَ ﴾
[الأحقَاف: 25]

Kuononga chinthu chilichonse ndi mphamvu ya Ambuye wake. Ndipo pamene kumacha m’mawa padalibe china chilichonse chooneka kupatula mabwinja a nyumba zawo. Mmenemo ndi mmene timalangira anthu ochita zoipa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: تدمر كل شيء بأمر ربها فأصبحوا لا يرى إلا مساكنهم كذلك نجزي, باللغة نيانجا

﴿تدمر كل شيء بأمر ربها فأصبحوا لا يرى إلا مساكنهم كذلك نجزي﴾ [الأحقَاف: 25]

Khaled Ibrahim Betala
“Yoononga chinthu chilichonse mwa lamulo la Mbuye wake!” Kenako adali osaonedwanso, kupatula nyumba zawo (ndizimene zidatsalira). Umo ndim’mene timawalipirira anthu oipa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek