Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahqaf ayat 5 - الأحقَاف - Page - Juz 26
﴿وَمَنۡ أَضَلُّ مِمَّن يَدۡعُواْ مِن دُونِ ٱللَّهِ مَن لَّا يَسۡتَجِيبُ لَهُۥٓ إِلَىٰ يَوۡمِ ٱلۡقِيَٰمَةِ وَهُمۡ عَن دُعَآئِهِمۡ غَٰفِلُونَ ﴾
[الأحقَاف: 5]
﴿ومن أضل ممن يدعو من دون الله من لا يستجيب له إلى﴾ [الأحقَاف: 5]
Khaled Ibrahim Betala “Kodi ndindani amene ali osokera kwambiri kuposa amene akupembedza zina kusiya Allah zomwe sizingathe kumuyankha mpaka tsiku la chiweruziro ndipo izo (zimafano) sizikuzindikira za mapemphero awo |