×

Nena, “Ine sindine woyamba mwa Atumwi ndipo sindidziwa chimene chingachitike kwa ine 46:9 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahqaf ⮕ (46:9) ayat 9 in Chichewa

46:9 Surah Al-Ahqaf ayat 9 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahqaf ayat 9 - الأحقَاف - Page - Juz 26

﴿قُلۡ مَا كُنتُ بِدۡعٗا مِّنَ ٱلرُّسُلِ وَمَآ أَدۡرِي مَا يُفۡعَلُ بِي وَلَا بِكُمۡۖ إِنۡ أَتَّبِعُ إِلَّا مَا يُوحَىٰٓ إِلَيَّ وَمَآ أَنَا۠ إِلَّا نَذِيرٞ مُّبِينٞ ﴾
[الأحقَاف: 9]

Nena, “Ine sindine woyamba mwa Atumwi ndipo sindidziwa chimene chingachitike kwa ine kapena kwa inu. Ine sinditsatira china chilichonse kupatula chokhacho chimene chavumbulutsidwa kwa ine. Ndipo ine sindili wina aliyense koma Mchenjezi basi.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل ما كنت بدعا من الرسل وما أدري ما يفعل بي ولا, باللغة نيانجا

﴿قل ما كنت بدعا من الرسل وما أدري ما يفعل بي ولا﴾ [الأحقَاف: 9]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Ine sindine woyamba pa aneneri, ndipo sindikudziwa zimene zidzachitike kwa ine ngakhale kwa inu. Sinditsatira koma zokhazo zimene zikuvumbulutsidwa kwa ine; ndipo ine sindili kanthu koma mchenjezi wolongosola (zofunika).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek