×

Nena: “Tandiuzani! Ngati uthengawu ndi wochokera kwa Mulungu ndipo inu muli kukana 46:10 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahqaf ⮕ (46:10) ayat 10 in Chichewa

46:10 Surah Al-Ahqaf ayat 10 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahqaf ayat 10 - الأحقَاف - Page - Juz 26

﴿قُلۡ أَرَءَيۡتُمۡ إِن كَانَ مِنۡ عِندِ ٱللَّهِ وَكَفَرۡتُم بِهِۦ وَشَهِدَ شَاهِدٞ مِّنۢ بَنِيٓ إِسۡرَٰٓءِيلَ عَلَىٰ مِثۡلِهِۦ فَـَٔامَنَ وَٱسۡتَكۡبَرۡتُمۡۚ إِنَّ ٱللَّهَ لَا يَهۡدِي ٱلۡقَوۡمَ ٱلظَّٰلِمِينَ ﴾
[الأحقَاف: 10]

Nena: “Tandiuzani! Ngati uthengawu ndi wochokera kwa Mulungu ndipo inu muli kukana kukhulupirira pamene mboni yochokera pakati pa ana a Israyeli yatsimikizira kuti Koraniyi ndi yochokera kwa Mulungu ndipo ndi yofanana. Motero iye adakhulupirira pamene inu muli kunyada. Ndithudi Mulungu satsogolera anthu ochita zoipa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل أرأيتم إن كان من عند الله وكفرتم به وشهد شاهد من, باللغة نيانجا

﴿قل أرأيتم إن كان من عند الله وكفرتم به وشهد شاهد من﴾ [الأحقَاف: 10]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Tandiuzani, ngati (buku ili) litachokera kwa Allah, ndipo inu nkulikana uku mboni yochokera mu ana a Israyeli itachitira umboni kuti idaliona longa limeneli, ndipo iyo nkulikhulupirira (bukuli) pomwe inu mwadzitukumula, ndithu Allah saongola anthu osalungama.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek