×

Iwo akadapirira mpaka pamene iwe udza kwa iwo, ndithudi, zikadakhala bwino ndipo 49:5 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hujurat ⮕ (49:5) ayat 5 in Chichewa

49:5 Surah Al-hujurat ayat 5 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hujurat ayat 5 - الحُجُرَات - Page - Juz 26

﴿وَلَوۡ أَنَّهُمۡ صَبَرُواْ حَتَّىٰ تَخۡرُجَ إِلَيۡهِمۡ لَكَانَ خَيۡرٗا لَّهُمۡۚ وَٱللَّهُ غَفُورٞ رَّحِيمٞ ﴾
[الحُجُرَات: 5]

Iwo akadapirira mpaka pamene iwe udza kwa iwo, ndithudi, zikadakhala bwino ndipo Mulungu ndi wokhululukira ndi wachisoni chosatha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولو أنهم صبروا حتى تخرج إليهم لكان خيرا لهم والله غفور رحيم, باللغة نيانجا

﴿ولو أنهم صبروا حتى تخرج إليهم لكان خيرا لهم والله غفور رحيم﴾ [الحُجُرَات: 5]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo iwo akadapirira ndi kuyembekeza (kuti) mpaka utuluke ndi kudza kwa iwo, zikadakhala zabwino kwa iwo; koma Allah Ngokhululuka kwabasi, Ngwachisoni chosatha
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek