×

Iye adati: “Ambuye wanga! Ine ndili ndi mphamvu pa ine mwini ndi 5:25 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:25) ayat 25 in Chichewa

5:25 Surah Al-Ma’idah ayat 25 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 25 - المَائدة - Page - Juz 6

﴿قَالَ رَبِّ إِنِّي لَآ أَمۡلِكُ إِلَّا نَفۡسِي وَأَخِيۖ فَٱفۡرُقۡ بَيۡنَنَا وَبَيۡنَ ٱلۡقَوۡمِ ٱلۡفَٰسِقِينَ ﴾
[المَائدة: 25]

Iye adati: “Ambuye wanga! Ine ndili ndi mphamvu pa ine mwini ndi pa mbale wanga, motero tipatuleni kugulu la anthu oswa malamulo.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال رب إني لا أملك إلا نفسي وأخي فافرق بيننا وبين القوم, باللغة نيانجا

﴿قال رب إني لا أملك إلا نفسي وأخي فافرق بيننا وبين القوم﴾ [المَائدة: 25]

Khaled Ibrahim Betala
“(Mûsa) adati: “E Mbuye wanga! Ndithudi, ine ndilibe nyonga (yokakamizira aliyense kutsatira lamulo Lanu) koma pa ine ndekha ndi pa m’bale wanga. Choncho tisiyanitseni ndi anthu awa opandukira chilamulo.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek