Quran with Chichewa translation - Surah Qaf ayat 37 - قٓ - Page - Juz 26
﴿إِنَّ فِي ذَٰلِكَ لَذِكۡرَىٰ لِمَن كَانَ لَهُۥ قَلۡبٌ أَوۡ أَلۡقَى ٱلسَّمۡعَ وَهُوَ شَهِيدٞ ﴾
[قٓ: 37]
﴿إن في ذلك لذكرى لمن كان له قلب أو ألقى السمع وهو﴾ [قٓ: 37]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu m’zimenezi muli chikumbutso kwa yemwe ali ndi mtima ndi yemwe akutchelera khutu (uku) iye ali pompo (ndi maganizo ake) |