Quran with Chichewa translation - Surah An-Najm ayat 52 - النَّجم - Page - Juz 27
﴿وَقَوۡمَ نُوحٖ مِّن قَبۡلُۖ إِنَّهُمۡ كَانُواْ هُمۡ أَظۡلَمَ وَأَطۡغَىٰ ﴾
[النَّجم: 52]
﴿وقوم نوح من قبل إنهم كانوا هم أظلم وأطغى﴾ [النَّجم: 52]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo (adawaononganso) anthu a Nuh, kale (asadaononge Âdi ndi Samudu). Ndithu iwo adali osalungama ndi olumpha malire kwambiri (kuposa Âdi ndi Samudu) |