×

Ndipo tidatumphutsa a kasupe padziko lapansi kotero madzi onse adakumana monga mwa 54:12 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qamar ⮕ (54:12) ayat 12 in Chichewa

54:12 Surah Al-Qamar ayat 12 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qamar ayat 12 - القَمَر - Page - Juz 27

﴿وَفَجَّرۡنَا ٱلۡأَرۡضَ عُيُونٗا فَٱلۡتَقَى ٱلۡمَآءُ عَلَىٰٓ أَمۡرٖ قَدۡ قُدِرَ ﴾
[القَمَر: 12]

Ndipo tidatumphutsa a kasupe padziko lapansi kotero madzi onse adakumana monga mwa lamulo lathu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وفجرنا الأرض عيونا فالتقى الماء على أمر قد قدر, باللغة نيانجا

﴿وفجرنا الأرض عيونا فالتقى الماء على أمر قد قدر﴾ [القَمَر: 12]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo tidaing’amba nthaka kukhala ndi akasupe (ofwamphuka madzi mwamphamvu). Choncho adakumana madzi (akumwamba ndi am’nthaka kuti awaononge) pamuyeso wopimidwa ndi kulamulidwa (ndi Allah)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek