Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qamar ayat 8 - القَمَر - Page - Juz 27
﴿مُّهۡطِعِينَ إِلَى ٱلدَّاعِۖ يَقُولُ ٱلۡكَٰفِرُونَ هَٰذَا يَوۡمٌ عَسِرٞ ﴾ 
[القَمَر: 8]
﴿مهطعين إلى الداع يقول الكافرون هذا يوم عسر﴾ [القَمَر: 8]
| Khaled Ibrahim Betala “Akuthamangira kwa woitana (uku atatukula mitu yawo, osatha kucheukira kwina). Adzanena osakhulupirira (tsiku lachiweruziro): “Ili nditsiku lovuta kwambiri.” |