Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Rahman ayat 46 - الرَّحمٰن - Page - Juz 27
﴿وَلِمَنۡ خَافَ مَقَامَ رَبِّهِۦ جَنَّتَانِ ﴾
[الرَّحمٰن: 46]
﴿ولمن خاف مقام ربه جنتان﴾ [الرَّحمٰن: 46]
Khaled Ibrahim Betala “Koma amene waopa kuti adzaimitsidwa kwa Mbuye wake (pa nthawi ya chiweruziro), adzalandira minda iwiri (yaikulu yamtendere) |