Quran with Chichewa translation - Surah Al-Waqi‘ah ayat 73 - الوَاقِعة - Page - Juz 27
﴿نَحۡنُ جَعَلۡنَٰهَا تَذۡكِرَةٗ وَمَتَٰعٗا لِّلۡمُقۡوِينَ ﴾
[الوَاقِعة: 73]
﴿نحن جعلناها تذكرة ومتاعا للمقوين﴾ [الوَاقِعة: 73]
Khaled Ibrahim Betala “Ife taupanga kuti ukhale chikumbutso (cha Moto watsiku lachimaliziro akauona), ndikuti ukhale chothandiza kwa anthu apaulendo (amene akuyenda m’chipululu) |