Quran with Chichewa translation - Surah Al-Waqi‘ah ayat 91 - الوَاقِعة - Page - Juz 27
﴿فَسَلَٰمٞ لَّكَ مِنۡ أَصۡحَٰبِ ٱلۡيَمِينِ ﴾
[الوَاقِعة: 91]
﴿فسلام لك من أصحاب اليمين﴾ [الوَاقِعة: 91]
Khaled Ibrahim Betala “(Kudzanenedwa kwa iye:) “Mtendere ukhale pa iwe, amene udali m’gulu la anthu akudzanja lakumanja (anthu abwino).” |