×

Palibe vuto limene limadza padziko kapena pa inu limene silinakhazikitsidwe kale Ife 57:22 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hadid ⮕ (57:22) ayat 22 in Chichewa

57:22 Surah Al-hadid ayat 22 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hadid ayat 22 - الحدِيد - Page - Juz 27

﴿مَآ أَصَابَ مِن مُّصِيبَةٖ فِي ٱلۡأَرۡضِ وَلَا فِيٓ أَنفُسِكُمۡ إِلَّا فِي كِتَٰبٖ مِّن قَبۡلِ أَن نَّبۡرَأَهَآۚ إِنَّ ذَٰلِكَ عَلَى ٱللَّهِ يَسِيرٞ ﴾
[الحدِيد: 22]

Palibe vuto limene limadza padziko kapena pa inu limene silinakhazikitsidwe kale Ife tisanalibweretse. Ndithudi chimenechi ndi chosavuta kwa Mulungu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ما أصاب من مصيبة في الأرض ولا في أنفسكم إلا في كتاب, باللغة نيانجا

﴿ما أصاب من مصيبة في الأرض ولا في أنفسكم إلا في كتاب﴾ [الحدِيد: 22]

Khaled Ibrahim Betala
“Silipezeka tsoka lililonse panthaka (monga chilala) ngakhale pamatupi anu koma lidalembedwa kale m’buku (la Allah) tisadalilenge ndi kulipereka. Ndithu zimenezo kwa Allah nzofewa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek