×

Kuti inu musakhumudwe chifukwa cha zinthu zabwino zimene simudazipeze kapena kunyada chifukwa 57:23 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hadid ⮕ (57:23) ayat 23 in Chichewa

57:23 Surah Al-hadid ayat 23 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hadid ayat 23 - الحدِيد - Page - Juz 27

﴿لِّكَيۡلَا تَأۡسَوۡاْ عَلَىٰ مَا فَاتَكُمۡ وَلَا تَفۡرَحُواْ بِمَآ ءَاتَىٰكُمۡۗ وَٱللَّهُ لَا يُحِبُّ كُلَّ مُخۡتَالٖ فَخُورٍ ﴾
[الحدِيد: 23]

Kuti inu musakhumudwe chifukwa cha zinthu zabwino zimene simudazipeze kapena kunyada chifukwa cha zokoma zimene zaperekedwa kwa inu. Mulungu sakonda anthu odzikundikira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لكيلا تأسوا على ما فاتكم ولا تفرحوا بما آتاكم والله لا يحب, باللغة نيانجا

﴿لكيلا تأسوا على ما فاتكم ولا تفرحوا بما آتاكم والله لا يحب﴾ [الحدِيد: 23]

Khaled Ibrahim Betala
“(Takudziwitsani zimenezi) kuti musadandaule ndi chimene chakudutsani, ndi kutinso musakondwere monyada ndi chimene wakupatsani. Allah sakonda aliyense wodzitama, wonyada
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek