Quran with Chichewa translation - Surah Al-hadid ayat 24 - الحدِيد - Page - Juz 27
﴿ٱلَّذِينَ يَبۡخَلُونَ وَيَأۡمُرُونَ ٱلنَّاسَ بِٱلۡبُخۡلِۗ وَمَن يَتَوَلَّ فَإِنَّ ٱللَّهَ هُوَ ٱلۡغَنِيُّ ٱلۡحَمِيدُ ﴾
[الحدِيد: 24]
﴿الذين يبخلون ويأمرون الناس بالبخل ومن يتول فإن الله هو الغني الحميد﴾ [الحدِيد: 24]
Khaled Ibrahim Betala “Amene akuchita umbombo (ndi chuma chawo; ndipo osapereka pa njira ya Allah) ndi kumalamula anthu ena kuchita umbombo. Ndipo amene atembenuke (adzalandira chilango chachikulu), ndithu Allah Ngolemera, (sasaukira chilichonse kwa wina), Ngotamandidwa |