×

Ndiye adalenga kumwamba ndi dziko lapansi m’masiku asanu ndi limodzi ndipo adabuka 57:4 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hadid ⮕ (57:4) ayat 4 in Chichewa

57:4 Surah Al-hadid ayat 4 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hadid ayat 4 - الحدِيد - Page - Juz 27

﴿هُوَ ٱلَّذِي خَلَقَ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضَ فِي سِتَّةِ أَيَّامٖ ثُمَّ ٱسۡتَوَىٰ عَلَى ٱلۡعَرۡشِۖ يَعۡلَمُ مَا يَلِجُ فِي ٱلۡأَرۡضِ وَمَا يَخۡرُجُ مِنۡهَا وَمَا يَنزِلُ مِنَ ٱلسَّمَآءِ وَمَا يَعۡرُجُ فِيهَاۖ وَهُوَ مَعَكُمۡ أَيۡنَ مَا كُنتُمۡۚ وَٱللَّهُ بِمَا تَعۡمَلُونَ بَصِيرٞ ﴾
[الحدِيد: 4]

Ndiye adalenga kumwamba ndi dziko lapansi m’masiku asanu ndi limodzi ndipo adabuka pa mwamba pa mpando wake wa Chifumu. Iye amadziwa chilichonse chimene chimalowa m’nthaka ndi chilichonse chimene chimatuluka mu iyo, zonse zimene zimadza pansi kuchokera kumwamba ndi zonse zimene zimakwera kumwamba. Ndipo Iye ali nanu kulikonse kumene mungakhale. Ndipo Mulungu amaona zonse zimene mumachita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: هو الذي خلق السموات والأرض في ستة أيام ثم استوى على العرش, باللغة نيانجا

﴿هو الذي خلق السموات والأرض في ستة أيام ثم استوى على العرش﴾ [الحدِيد: 4]

Khaled Ibrahim Betala
“Iye ndi Amene adalenga kumwamba ndi pansi (ndi zonse zammenemo) m’masiku asanu ndi limodzi kenako adakhazikika pa Arsh (Mpando Wake wachifumu monga momwe Iye adziwira polongosola ufumu Wake). Akudziwa chilichonse cholowa m’nthaka ndi chimene chikutuluka m’menemo; ndi chilichonse chimene chikutsika kuchokera kumwamba ndi chimene chikukwera kumeneko. Ndipo Iye ali nanu paliponse pamene muli. Ndithu Allah amaona chilichonse chimene mukuchita, (sichibisika chilichonse kwa Iye)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek