Quran with Chichewa translation - Surah Al-hadid ayat 3 - الحدِيد - Page - Juz 27
﴿هُوَ ٱلۡأَوَّلُ وَٱلۡأٓخِرُ وَٱلظَّٰهِرُ وَٱلۡبَاطِنُۖ وَهُوَ بِكُلِّ شَيۡءٍ عَلِيمٌ ﴾
[الحدِيد: 3]
﴿هو الأول والآخر والظاهر والباطن وهو بكل شيء عليم﴾ [الحدِيد: 3]
Khaled Ibrahim Betala “Iye ndi Oyamba (adalipo chilichonse chisadayambe); Wamuyaya (zonse zikadzatha); Woonekera (mzisonyezo pa chinthu chilichonse), Wobisika mkati kwambiri (saonedwa ndi maso pamoyo uno), Iye Ngodziwa chilichonse (kunja ndi mkati mwake) |