×

Ndithudi ngati iwo apirikitsidwa, iwo sadzapita nawo ayi ndipo ngati inu muputidwa 59:12 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hashr ⮕ (59:12) ayat 12 in Chichewa

59:12 Surah Al-hashr ayat 12 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hashr ayat 12 - الحَشر - Page - Juz 28

﴿لَئِنۡ أُخۡرِجُواْ لَا يَخۡرُجُونَ مَعَهُمۡ وَلَئِن قُوتِلُواْ لَا يَنصُرُونَهُمۡ وَلَئِن نَّصَرُوهُمۡ لَيُوَلُّنَّ ٱلۡأَدۡبَٰرَ ثُمَّ لَا يُنصَرُونَ ﴾
[الحَشر: 12]

Ndithudi ngati iwo apirikitsidwa, iwo sadzapita nawo ayi ndipo ngati inu muputidwa iwo sadzakuthandizani konsekonse. Ndipo ngati iwo atathandiza, iwo adzangobwerera m’mbuyo motero iwo sadzapambana ai

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لئن أخرجوا لا يخرجون معهم ولئن قوتلوا لا ينصرونهم ولئن نصروهم ليولن, باللغة نيانجا

﴿لئن أخرجوا لا يخرجون معهم ولئن قوتلوا لا ينصرونهم ولئن نصروهم ليولن﴾ [الحَشر: 12]

Khaled Ibrahim Betala
“Ngati atatulutsidwa, sangatuluke nawo limodzi; ngati atamenyedwa, sangawathandize ndipo ngati atawathandiza atembenuza misana (kuthawa) kenako sapulumutsidwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek