Quran with Chichewa translation - Surah Al-hashr ayat 13 - الحَشر - Page - Juz 28
﴿لَأَنتُمۡ أَشَدُّ رَهۡبَةٗ فِي صُدُورِهِم مِّنَ ٱللَّهِۚ ذَٰلِكَ بِأَنَّهُمۡ قَوۡمٞ لَّا يَفۡقَهُونَ ﴾
[الحَشر: 13]
﴿لأنتم أشد رهبة في صدورهم من الله ذلك بأنهم قوم لا يفقهون﴾ [الحَشر: 13]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu inu (Asilamu) mukuopedwa kwambiri m’mitima mwawo kuposa mmene akumuopera Allah. Zimenezo nchifukwa chakuti iwo ndi anthu osazindikira (chilichonse) |