Quran with Chichewa translation - Surah Al-hashr ayat 6 - الحَشر - Page - Juz 28
﴿وَمَآ أَفَآءَ ٱللَّهُ عَلَىٰ رَسُولِهِۦ مِنۡهُمۡ فَمَآ أَوۡجَفۡتُمۡ عَلَيۡهِ مِنۡ خَيۡلٖ وَلَا رِكَابٖ وَلَٰكِنَّ ٱللَّهَ يُسَلِّطُ رُسُلَهُۥ عَلَىٰ مَن يَشَآءُۚ وَٱللَّهُ عَلَىٰ كُلِّ شَيۡءٖ قَدِيرٞ ﴾
[الحَشر: 6]
﴿وما أفاء الله على رسوله منهم فما أوجفتم عليه من خيل ولا﴾ [الحَشر: 6]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo chuma chimene wapereka Allah kwa Mtumiki Wake chochokera kwa iwo (Bani Nadhiri), chimenecho inu simudathamangitse mahachi kapena ngamira (pakuchipeza), koma Allah amapereka mphamvu kwa atumiki Ake zogonjetsera amene wamfuna. Ndipo Allah ali ndi Mphamvu (pa) chilichonse |