Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 17 - الأنعَام - Page - Juz 7
﴿وَإِن يَمۡسَسۡكَ ٱللَّهُ بِضُرّٖ فَلَا كَاشِفَ لَهُۥٓ إِلَّا هُوَۖ وَإِن يَمۡسَسۡكَ بِخَيۡرٖ فَهُوَ عَلَىٰ كُلِّ شَيۡءٖ قَدِيرٞ ﴾
[الأنعَام: 17]
﴿وإن يمسسك الله بضر فلا كاشف له إلا هو وإن يمسسك بخير﴾ [الأنعَام: 17]
Khaled Ibrahim Betala “Ngati Allah atakukhudza ndi mazunzo, palibe aliyense angathe kukuchotsera, koma Iye basi; ndipo ngati atakukhudza ndi zabwino (palibe amene angakutsekereze ku zabwinozo). Iye ali ndi mphamvu pa chilichonse |