×

Koma zonse zimene adali kuzibisa kale zidzaonekera poyera kwa iwo. Komabe akadabwezedwa, 6:28 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-An‘am ⮕ (6:28) ayat 28 in Chichewa

6:28 Surah Al-An‘am ayat 28 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 28 - الأنعَام - Page - Juz 7

﴿بَلۡ بَدَا لَهُم مَّا كَانُواْ يُخۡفُونَ مِن قَبۡلُۖ وَلَوۡ رُدُّواْ لَعَادُواْ لِمَا نُهُواْ عَنۡهُ وَإِنَّهُمۡ لَكَٰذِبُونَ ﴾
[الأنعَام: 28]

Koma zonse zimene adali kuzibisa kale zidzaonekera poyera kwa iwo. Komabe akadabwezedwa, iwo akadakabwerera ku zinthu zimene adaletsedwa. Ndithudi iwo ndi anthu a bodza

❮ Previous Next ❯

ترجمة: بل بدا لهم ما كانوا يخفون من قبل ولو ردوا لعادوا لما, باللغة نيانجا

﴿بل بدا لهم ما كانوا يخفون من قبل ولو ردوا لعادوا لما﴾ [الأنعَام: 28]

Khaled Ibrahim Betala
“(Sichoncho) koma zawaonekera poyera zomwe adali kubisa kale. Ndipo akadabwezedwa akadabwerezanso kuchita zimene adaletsedwa. Ndithudi iwo ngabodza basi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek