×

Iwo adanenetsa kuti: “Kulibenso moyo wina uliwonse kupatula moyo wathu wadziko lapansi 6:29 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-An‘am ⮕ (6:29) ayat 29 in Chichewa

6:29 Surah Al-An‘am ayat 29 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 29 - الأنعَام - Page - Juz 7

﴿وَقَالُوٓاْ إِنۡ هِيَ إِلَّا حَيَاتُنَا ٱلدُّنۡيَا وَمَا نَحۡنُ بِمَبۡعُوثِينَ ﴾
[الأنعَام: 29]

Iwo adanenetsa kuti: “Kulibenso moyo wina uliwonse kupatula moyo wathu wadziko lapansi ndiponso ife sitidzaukitsidwa kwa akufa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقالوا إن هي إلا حياتنا الدنيا وما نحن بمبعوثين, باللغة نيانجا

﴿وقالوا إن هي إلا حياتنا الدنيا وما نحن بمبعوثين﴾ [الأنعَام: 29]

Khaled Ibrahim Betala
“Akumanena: “Palibe moyo wina koma moyo wathu wa pa dziko lapansi basi. Ndipo ife sitidzaukitsidwanso m’manda.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek