Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 58 - الأنعَام - Page - Juz 7
﴿قُل لَّوۡ أَنَّ عِندِي مَا تَسۡتَعۡجِلُونَ بِهِۦ لَقُضِيَ ٱلۡأَمۡرُ بَيۡنِي وَبَيۡنَكُمۡۗ وَٱللَّهُ أَعۡلَمُ بِٱلظَّٰلِمِينَ ﴾
[الأنعَام: 58]
﴿قل لو أن عندي ما تستعجلون به لقضي الأمر بيني وبينكم والله﴾ [الأنعَام: 58]
Khaled Ibrahim Betala “Nena: “Ndikadakhala nacho chimene mukuchifulumizitsacho, ndiye kuti chinthucho chikadachitika pakati pa ine ndi inu (ndikadakuonongani koma ndilibe nyonga). Ndipo Allah akuwadziwa bwino anthu ochita zoipa.” |