×

Iye amadziwa chilichonse chimene chili kumwamba ndi padziko lapansi ndipo amadziwa zonse 64:4 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taghabun ⮕ (64:4) ayat 4 in Chichewa

64:4 Surah At-Taghabun ayat 4 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taghabun ayat 4 - التغَابُن - Page - Juz 28

﴿يَعۡلَمُ مَا فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِ وَيَعۡلَمُ مَا تُسِرُّونَ وَمَا تُعۡلِنُونَۚ وَٱللَّهُ عَلِيمُۢ بِذَاتِ ٱلصُّدُورِ ﴾
[التغَابُن: 4]

Iye amadziwa chilichonse chimene chili kumwamba ndi padziko lapansi ndipo amadziwa zonse zimene mumabisa ndi zimene mumaulula. Ndithudi Mulungu amadziwa bwino lomwe zinsinsi za m’mitima mwanu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: يعلم ما في السموات والأرض ويعلم ما تسرون وما تعلنون والله عليم, باللغة نيانجا

﴿يعلم ما في السموات والأرض ويعلم ما تسرون وما تعلنون والله عليم﴾ [التغَابُن: 4]

Khaled Ibrahim Betala
“(Allah) akudziwa za kumwamba ndi za m’dziko lapansi, ndiponso akudziwa zimene mukuzibisa ndi zimene mukuzilengeza (zochita ndi zoyankhula); Allah Ngodziwa za m’zifuwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek