×

Ndipo ngati iwo ali pafupi kukwaniritsa nthawi yawo, mukhoza kuwasunga mwaubwino kapena 65:2 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah AT-Talaq ⮕ (65:2) ayat 2 in Chichewa

65:2 Surah AT-Talaq ayat 2 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah AT-Talaq ayat 2 - الطَّلَاق - Page - Juz 28

﴿فَإِذَا بَلَغۡنَ أَجَلَهُنَّ فَأَمۡسِكُوهُنَّ بِمَعۡرُوفٍ أَوۡ فَارِقُوهُنَّ بِمَعۡرُوفٖ وَأَشۡهِدُواْ ذَوَيۡ عَدۡلٖ مِّنكُمۡ وَأَقِيمُواْ ٱلشَّهَٰدَةَ لِلَّهِۚ ذَٰلِكُمۡ يُوعَظُ بِهِۦ مَن كَانَ يُؤۡمِنُ بِٱللَّهِ وَٱلۡيَوۡمِ ٱلۡأٓخِرِۚ وَمَن يَتَّقِ ٱللَّهَ يَجۡعَل لَّهُۥ مَخۡرَجٗا ﴾
[الطَّلَاق: 2]

Ndipo ngati iwo ali pafupi kukwaniritsa nthawi yawo, mukhoza kuwasunga mwaubwino kapena kuwasiya mwaulemu. Ndipo itanani mboni ziwiri za chilungamo kuchokera pakati panu. Ndipo perekani umboni wanu chifukwa cha Mulungu. Limeneli ndi langizo limene laperekedwa kwa iye amene amakhulupirira mwa Mulungu ndi tsiku lomaliza. Ndipo aliyense amene aopa Mulungu, Iye adzamupulumutsa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فإذا بلغن أجلهن فأمسكوهن بمعروف أو فارقوهن بمعروف وأشهدوا ذوي عدل منكم, باللغة نيانجا

﴿فإذا بلغن أجلهن فأمسكوهن بمعروف أو فارقوهن بمعروف وأشهدوا ذوي عدل منكم﴾ [الطَّلَاق: 2]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho pamene iwo (osiyidwawo) nyengo yawo (Edda) itayandikira kutha, abwelereni mwa ubwino kapena asiyeni mwaubwino (polekelera nyengoyo kuti ithe); ndipo (powabwerera) funani mboni ziwiri zolungama zochokera mwa inu (zimene zichitire umboni kuti inu mukubwererana) ndipo perekani umboni chifukwa choopa Allah. Zimenezo ndizo akulangizidwa nazo amene akhulupirira mwa Allah ndi tsiku lachimaliziro. Ndipo amene akumuopa Allah (potsatira malamulo Ake), amkonzera njira yotulukira (m’mavuto)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek