×

سورة الطلاق باللغة نيانجا

ترجمات القرآنباللغة نيانجا ⬅ سورة الطلاق

ترجمة معاني سورة الطلاق باللغة نيانجا - Chichewa

القرآن باللغة نيانجا - سورة الطلاق مترجمة إلى اللغة نيانجا، Surah Talaq in Chichewa. نوفر ترجمة دقيقة سورة الطلاق باللغة نيانجا - Chichewa, الآيات 12 - رقم السورة 65 - الصفحة 558.

بسم الله الرحمن الرحيم

يَا أَيُّهَا النَّبِيُّ إِذَا طَلَّقْتُمُ النِّسَاءَ فَطَلِّقُوهُنَّ لِعِدَّتِهِنَّ وَأَحْصُوا الْعِدَّةَ ۖ وَاتَّقُوا اللَّهَ رَبَّكُمْ ۖ لَا تُخْرِجُوهُنَّ مِن بُيُوتِهِنَّ وَلَا يَخْرُجْنَ إِلَّا أَن يَأْتِينَ بِفَاحِشَةٍ مُّبَيِّنَةٍ ۚ وَتِلْكَ حُدُودُ اللَّهِ ۚ وَمَن يَتَعَدَّ حُدُودَ اللَّهِ فَقَدْ ظَلَمَ نَفْسَهُ ۚ لَا تَدْرِي لَعَلَّ اللَّهَ يُحْدِثُ بَعْدَ ذَٰلِكَ أَمْرًا (1)
Oh iwe Mtumwi! Ngati usudzula akazi ako, asudzule potsatira nthawi zawo. Ndipo werenga bwino bwino masiku awo. Ndipo opani Mulungu Ambuye wanu ndipo musawapirikitse m’nyumba zawo ndipo iwo asachoke pokhapokha ngati iwo apalamula mlandu wachigololo. Amenewa ndiwo malamulo amene akhazikitsidwa ndi Mulungu. Ndipo aliyense amene aphwanya malamulo a Mulungu, ndithudi, amapondereza mzimu wake. Inu Al Talaq 605 simudziwa kuti, mwina, Mulungu adzakukumanizaninso
فَإِذَا بَلَغْنَ أَجَلَهُنَّ فَأَمْسِكُوهُنَّ بِمَعْرُوفٍ أَوْ فَارِقُوهُنَّ بِمَعْرُوفٍ وَأَشْهِدُوا ذَوَيْ عَدْلٍ مِّنكُمْ وَأَقِيمُوا الشَّهَادَةَ لِلَّهِ ۚ ذَٰلِكُمْ يُوعَظُ بِهِ مَن كَانَ يُؤْمِنُ بِاللَّهِ وَالْيَوْمِ الْآخِرِ ۚ وَمَن يَتَّقِ اللَّهَ يَجْعَل لَّهُ مَخْرَجًا (2)
Ndipo ngati iwo ali pafupi kukwaniritsa nthawi yawo, mukhoza kuwasunga mwaubwino kapena kuwasiya mwaulemu. Ndipo itanani mboni ziwiri za chilungamo kuchokera pakati panu. Ndipo perekani umboni wanu chifukwa cha Mulungu. Limeneli ndi langizo limene laperekedwa kwa iye amene amakhulupirira mwa Mulungu ndi tsiku lomaliza. Ndipo aliyense amene aopa Mulungu, Iye adzamupulumutsa
وَيَرْزُقْهُ مِنْ حَيْثُ لَا يَحْتَسِبُ ۚ وَمَن يَتَوَكَّلْ عَلَى اللَّهِ فَهُوَ حَسْبُهُ ۚ إِنَّ اللَّهَ بَالِغُ أَمْرِهِ ۚ قَدْ جَعَلَ اللَّهُ لِكُلِّ شَيْءٍ قَدْرًا (3)
Ndipo Iye adzamupatsa zinthu kuchokera ku mbali imene sanali kuyembekeza. Ndipo aliyense amene amakhulupirira mwa Mulungu, Iye adzamupatsa chili chonse. Mulungu, ndithudi, adzamupatsa iye zofuna zake zonse. Ndithudi Mulungu adakhazikitsa muyeso wa chilichonse
وَاللَّائِي يَئِسْنَ مِنَ الْمَحِيضِ مِن نِّسَائِكُمْ إِنِ ارْتَبْتُمْ فَعِدَّتُهُنَّ ثَلَاثَةُ أَشْهُرٍ وَاللَّائِي لَمْ يَحِضْنَ ۚ وَأُولَاتُ الْأَحْمَالِ أَجَلُهُنَّ أَن يَضَعْنَ حَمْلَهُنَّ ۚ وَمَن يَتَّقِ اللَّهَ يَجْعَل لَّهُ مِنْ أَمْرِهِ يُسْرًا (4)
Ndipo ena akazi anu amene adasiya kupita kumwezi, kwa iwo nthawi yawo yodikira, ngati inu mukaika, ndi miyezi itatu ndipo iwo amene anasiyiratu, nthawi yawo idzakhala chimodzimodzi. Ndipo iwo amene ali ndi akazi odwala pakati, nthawi yawo idzakhala mpaka pamene abereka. Ndipo aliyense amene amaopa Mulungu, Iye adzamuchepetsera mavuto ake
ذَٰلِكَ أَمْرُ اللَّهِ أَنزَلَهُ إِلَيْكُمْ ۚ وَمَن يَتَّقِ اللَّهَ يُكَفِّرْ عَنْهُ سَيِّئَاتِهِ وَيُعْظِمْ لَهُ أَجْرًا (5)
Uwu ndi ulamuliro wa Mulungu umene wakutumizirani inu. Ndipo aliyense amene aopa Mulungu, Iye adzamuchotsera zoipa zake. Ndipo Iye adzamuchulukitsira mphotho yake
أَسْكِنُوهُنَّ مِنْ حَيْثُ سَكَنتُم مِّن وُجْدِكُمْ وَلَا تُضَارُّوهُنَّ لِتُضَيِّقُوا عَلَيْهِنَّ ۚ وَإِن كُنَّ أُولَاتِ حَمْلٍ فَأَنفِقُوا عَلَيْهِنَّ حَتَّىٰ يَضَعْنَ حَمْلَهُنَّ ۚ فَإِنْ أَرْضَعْنَ لَكُمْ فَآتُوهُنَّ أُجُورَهُنَّ ۖ وَأْتَمِرُوا بَيْنَكُم بِمَعْرُوفٍ ۖ وَإِن تَعَاسَرْتُمْ فَسَتُرْضِعُ لَهُ أُخْرَىٰ (6)
Khalani nawo monga momwe inu muli kukhalira, molingana ndi kupeza kwanu. Musawazunze ndi cholinga chowasowetsa mtendere. Ngati iwo ali ndi pakati, asamalireni mpaka pamene iwo abereka. Ndipo ngati iwo ali kuyamwitsa, apatseni malipiro awo ndipo lemekezanani. Ndipo ngati pali mavuto oti simuli kugwirizana m’banja, pezani Mayi wina kuti ayamwitse mwana m’malo mwake
لِيُنفِقْ ذُو سَعَةٍ مِّن سَعَتِهِ ۖ وَمَن قُدِرَ عَلَيْهِ رِزْقُهُ فَلْيُنفِقْ مِمَّا آتَاهُ اللَّهُ ۚ لَا يُكَلِّفُ اللَّهُ نَفْسًا إِلَّا مَا آتَاهَا ۚ سَيَجْعَلُ اللَّهُ بَعْدَ عُسْرٍ يُسْرًا (7)
Mulekeni munthu wolemera kuti apereke molingana ndi chuma chake ndipo munthu wosauka molingana ndi mmene Mulungu adamupatsira iye. Mulungu sakhazika mtulo wolemera pa munthu umene sangathe kuunyamula. Mulungu adzapereka mtendere mavuto akatha
وَكَأَيِّن مِّن قَرْيَةٍ عَتَتْ عَنْ أَمْرِ رَبِّهَا وَرُسُلِهِ فَحَاسَبْنَاهَا حِسَابًا شَدِيدًا وَعَذَّبْنَاهَا عَذَابًا نُّكْرًا (8)
Ndipo ndi mizinda yambiri imene idaukira malamulo a Mulungu ndi Atumwi ndipo Ife tidayilanga iyo ndipo tidzailanga ndi chilango choopsa zedi
فَذَاقَتْ وَبَالَ أَمْرِهَا وَكَانَ عَاقِبَةُ أَمْرِهَا خُسْرًا (9)
Motero iyo idalawa mphotho ya kusakhulupilira kwake ndipo mapeto a kusakhulupilira adali chionongeko
أَعَدَّ اللَّهُ لَهُمْ عَذَابًا شَدِيدًا ۖ فَاتَّقُوا اللَّهَ يَا أُولِي الْأَلْبَابِ الَّذِينَ آمَنُوا ۚ قَدْ أَنزَلَ اللَّهُ إِلَيْكُمْ ذِكْرًا (10)
Mulungu wawakonzeraiwochilangochoopsa. Moteroopani Mulungu oh inu anthu ozindikira! Inu amene mwakhulupirira, ndithudi, Mulungu watumiza chikumbutso kwa inu
رَّسُولًا يَتْلُو عَلَيْكُمْ آيَاتِ اللَّهِ مُبَيِّنَاتٍ لِّيُخْرِجَ الَّذِينَ آمَنُوا وَعَمِلُوا الصَّالِحَاتِ مِنَ الظُّلُمَاتِ إِلَى النُّورِ ۚ وَمَن يُؤْمِن بِاللَّهِ وَيَعْمَلْ صَالِحًا يُدْخِلْهُ جَنَّاتٍ تَجْرِي مِن تَحْتِهَا الْأَنْهَارُ خَالِدِينَ فِيهَا أَبَدًا ۖ قَدْ أَحْسَنَ اللَّهُ لَهُ رِزْقًا (11)
Mtumwi amene ali kukuuzani zizindikiro zooneka za Mulungu ndi cholinga choti atsogolere onse amene akhulupirira ndipo amachita ntchito zabwino kuchokera ku mdima kupita kowala. Ndipo aliyense amene amakhulupirira mwa Mulungu ndipo amachita ntchito zabwino, Iye adzamulowetsa m’minda imene pansi pake pamayenda mitsinje kuti adzakhaleko mpaka kalekale. Ndithudi Mulungu wawapatsa iwo mphotho yabwino kwambiri
اللَّهُ الَّذِي خَلَقَ سَبْعَ سَمَاوَاتٍ وَمِنَ الْأَرْضِ مِثْلَهُنَّ يَتَنَزَّلُ الْأَمْرُ بَيْنَهُنَّ لِتَعْلَمُوا أَنَّ اللَّهَ عَلَىٰ كُلِّ شَيْءٍ قَدِيرٌ وَأَنَّ اللَّهَ قَدْ أَحَاطَ بِكُلِّ شَيْءٍ عِلْمًا (12)
Ndi Mulungu amene adalenga miyamba isanu ndi iwiri ndi dziko lapansi lolingana nayo. Malamulo ake amatsatiridwa ndi izo kuti inu mukhoza kudziwa kuti Mulungu ali ndi mphamvu pa zinthu zonse ndipo kuti Mulungu amadziwa chilichonse
❮ السورة السابقة السورة التـالية ❯

قراءة المزيد من سور القرآن الكريم :

1- الفاتحة2- البقرة3- آل عمران
4- النساء5- المائدة6- الأنعام
7- الأعراف8- الأنفال9- التوبة
10- يونس11- هود12- يوسف
13- الرعد14- إبراهيم15- الحجر
16- النحل17- الإسراء18- الكهف
19- مريم20- طه21- الأنبياء
22- الحج23- المؤمنون24- النور
25- الفرقان26- الشعراء27- النمل
28- القصص29- العنكبوت30- الروم
31- لقمان32- السجدة33- الأحزاب
34- سبأ35- فاطر36- يس
37- الصافات38- ص39- الزمر
40- غافر41- فصلت42- الشورى
43- الزخرف44- الدخان45- الجاثية
46- الأحقاف47- محمد48- الفتح
49- الحجرات50- ق51- الذاريات
52- الطور53- النجم54- القمر
55- الرحمن56- الواقعة57- الحديد
58- المجادلة59- الحشر60- الممتحنة
61- الصف62- الجمعة63- المنافقون
64- التغابن65- الطلاق66- التحريم
67- الملك68- القلم69- الحاقة
70- المعارج71- نوح72- الجن
73- المزمل74- المدثر75- القيامة
76- الإنسان77- المرسلات78- النبأ
79- النازعات80- عبس81- التكوير
82- الإنفطار83- المطففين84- الانشقاق
85- البروج86- الطارق87- الأعلى
88- الغاشية89- الفجر90- البلد
91- الشمس92- الليل93- الضحى
94- الشرح95- التين96- العلق
97- القدر98- البينة99- الزلزلة
100- العاديات101- القارعة102- التكاثر
103- العصر104- الهمزة105- الفيل
106- قريش107- الماعون108- الكوثر
109- الكافرون110- النصر111- المسد
112- الإخلاص113- الفلق114- الناس