Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mulk ayat 10 - المُلك - Page - Juz 29
﴿وَقَالُواْ لَوۡ كُنَّا نَسۡمَعُ أَوۡ نَعۡقِلُ مَا كُنَّا فِيٓ أَصۡحَٰبِ ٱلسَّعِيرِ ﴾
[المُلك: 10]
﴿وقالوا لو كنا نسمع أو نعقل ما كنا في أصحاب السعير﴾ [المُلك: 10]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo adzanena: “Tikadakhala kuti tidamvera (zimene ankatiuza) kapena kuziganizira mwanzeru sitikadakhala m’gulu la anthu a ku Moto.” |