×

Kodiiwosaonambalamezimenezimaulukapamwamba pawo, zikutambasula ndi kutseka mapiko awo? Palibe chimene chimazigwira kupatula Mwini 67:19 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Mulk ⮕ (67:19) ayat 19 in Chichewa

67:19 Surah Al-Mulk ayat 19 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mulk ayat 19 - المُلك - Page - Juz 29

﴿أَوَلَمۡ يَرَوۡاْ إِلَى ٱلطَّيۡرِ فَوۡقَهُمۡ صَٰٓفَّٰتٖ وَيَقۡبِضۡنَۚ مَا يُمۡسِكُهُنَّ إِلَّا ٱلرَّحۡمَٰنُۚ إِنَّهُۥ بِكُلِّ شَيۡءِۭ بَصِيرٌ ﴾
[المُلك: 19]

Kodiiwosaonambalamezimenezimaulukapamwamba pawo, zikutambasula ndi kutseka mapiko awo? Palibe chimene chimazigwira kupatula Mwini chisoni chosatha. Ndithudi Iye amaona chilichonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أو لم يروا إلى الطير فوقهم صافات ويقبضن ما يمسكهن إلا الرحمن, باللغة نيانجا

﴿أو لم يروا إلى الطير فوقهم صافات ويقبضن ما يمسكهن إلا الرحمن﴾ [المُلك: 19]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi, sadaone mbalame pamwamba pawo mmene zikutambasulira (mapiko ake) ndi kuwafumbata. Palibe amene akuzigwira kuti zisagwe koma (Allah) Wachifundo chambiri; ndithudi Iye pachilichonse Ngopenya
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek