Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mulk ayat 29 - المُلك - Page - Juz 29
﴿قُلۡ هُوَ ٱلرَّحۡمَٰنُ ءَامَنَّا بِهِۦ وَعَلَيۡهِ تَوَكَّلۡنَاۖ فَسَتَعۡلَمُونَ مَنۡ هُوَ فِي ضَلَٰلٖ مُّبِينٖ ﴾
[المُلك: 29]
﴿قل هو الرحمن آمنا به وعليه توكلنا فستعلمون من هو في ضلال﴾ [المُلك: 29]
Khaled Ibrahim Betala “Nena: “Iye ndiye (Allah) Wachifundo chambiri, takhulupirira mwa Iye ndiponso kwa Iye ndikumene tatsamira. Choncho posachedwapa mudziwa (chilango chikatsika kuti) ndani (m’magulu awiriwa) yemwe ali m’kusokera koonekera.” |