Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mulk ayat 28 - المُلك - Page - Juz 29
﴿قُلۡ أَرَءَيۡتُمۡ إِنۡ أَهۡلَكَنِيَ ٱللَّهُ وَمَن مَّعِيَ أَوۡ رَحِمَنَا فَمَن يُجِيرُ ٱلۡكَٰفِرِينَ مِنۡ عَذَابٍ أَلِيمٖ ﴾
[المُلك: 28]
﴿قل أرأيتم إن أهلكني الله ومن معي أو رحمنا فمن يجير الكافرين﴾ [المُلك: 28]
Khaled Ibrahim Betala “Nena (iwe Mtumiki{s.a.w}): “Tandiuzani ngati Allah atandiononga pamodzi ndi amene ndili nawo (monga momwe mukufunira) kapena kutichitira chifundo (ndikutalikitsa nthawi ya moyo wathu). Nanga ndani amene adzawateteza wosakhulupirira ku chilango chowawa?” |