Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qalam ayat 28 - القَلَم - Page - Juz 29
﴿قَالَ أَوۡسَطُهُمۡ أَلَمۡ أَقُل لَّكُمۡ لَوۡلَا تُسَبِّحُونَ ﴾
[القَلَم: 28]
﴿قال أوسطهم ألم أقل لكم لولا تسبحون﴾ [القَلَم: 28]
Khaled Ibrahim Betala “Wolungama mwa iwo adanena: “Kodi sindinakuuzeni (pamene mudali kulangizana zomana osowa) kuti bwanji osamkumbukira Allah (ndi kusintha cholinga chanu)?” |