Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qalam ayat 33 - القَلَم - Page - Juz 29
﴿كَذَٰلِكَ ٱلۡعَذَابُۖ وَلَعَذَابُ ٱلۡأٓخِرَةِ أَكۡبَرُۚ لَوۡ كَانُواْ يَعۡلَمُونَ ﴾
[القَلَم: 33]
﴿كذلك العذاب ولعذاب الآخرة أكبر لو كانوا يعلمون﴾ [القَلَم: 33]
Khaled Ibrahim Betala “Umo ndi mmene chimakhalira chilango (Changa chomwe ndimachitsitsa pa dziko lapansi kwa amene chamuyenera); koma chilango cha tsiku lachimaliziro nchachikulu zedi, akadakhala akudziwa |