×

Ndithudi amene amati zizindikiro zathu ndi zabodza ndipo amazinyoza izo, makomo a 7:40 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:40) ayat 40 in Chichewa

7:40 Surah Al-A‘raf ayat 40 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 40 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿إِنَّ ٱلَّذِينَ كَذَّبُواْ بِـَٔايَٰتِنَا وَٱسۡتَكۡبَرُواْ عَنۡهَا لَا تُفَتَّحُ لَهُمۡ أَبۡوَٰبُ ٱلسَّمَآءِ وَلَا يَدۡخُلُونَ ٱلۡجَنَّةَ حَتَّىٰ يَلِجَ ٱلۡجَمَلُ فِي سَمِّ ٱلۡخِيَاطِۚ وَكَذَٰلِكَ نَجۡزِي ٱلۡمُجۡرِمِينَ ﴾
[الأعرَاف: 40]

Ndithudi amene amati zizindikiro zathu ndi zabodza ndipo amazinyoza izo, makomo a kumwamba sadzatsegulidwa kwa iwo ndipo iwo sadzalowa ku Paradiso pokhapokha ngati ngamira italowa pa diso la zingano. Mmenemo ndi mmene timalipirira anthu ochita zoipa malipiro awo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الذين كذبوا بآياتنا واستكبروا عنها لا تفتح لهم أبواب السماء ولا, باللغة نيانجا

﴿إن الذين كذبوا بآياتنا واستكبروا عنها لا تفتح لهم أبواب السماء ولا﴾ [الأعرَاف: 40]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithudi, amene akutsutsa zivumbulutso Zathu nadzitukumula nazo (pakukana kuzitsata), sadzatsekulidwa kwa iwo makomo a kumwamba, ndipo sadzalowa ku Munda wamtendere mpaka ngamira idzalowe pa bowo la singano. Umo ndimomwe timawalipirira anthu ochimwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek