×

Ndipo m’badwo woyamba udzati kwa m’badwo womaliza, “Inu simunachite zabwino kuposa ife 7:39 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:39) ayat 39 in Chichewa

7:39 Surah Al-A‘raf ayat 39 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 39 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿وَقَالَتۡ أُولَىٰهُمۡ لِأُخۡرَىٰهُمۡ فَمَا كَانَ لَكُمۡ عَلَيۡنَا مِن فَضۡلٖ فَذُوقُواْ ٱلۡعَذَابَ بِمَا كُنتُمۡ تَكۡسِبُونَ ﴾
[الأعرَاف: 39]

Ndipo m’badwo woyamba udzati kwa m’badwo womaliza, “Inu simunachite zabwino kuposa ife motero lawani chilango cha ntchito zanu zimene mudali kuchita.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقالت أولاهم لأخراهم فما كان لكم علينا من فضل فذوقوا العذاب بما, باللغة نيانجا

﴿وقالت أولاهم لأخراهم فما كان لكم علينا من فضل فذوقوا العذاب بما﴾ [الأعرَاف: 39]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo oyamba awo adzati kwa otsiriza awo: “Inunso mudalibe ubwino woposa ife; choncho, lawani chilango cha zomwe mudapeza (m’zochitachita zanu).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek