Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 42 - الأعرَاف - Page - Juz 8
﴿وَٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَعَمِلُواْ ٱلصَّٰلِحَٰتِ لَا نُكَلِّفُ نَفۡسًا إِلَّا وُسۡعَهَآ أُوْلَٰٓئِكَ أَصۡحَٰبُ ٱلۡجَنَّةِۖ هُمۡ فِيهَا خَٰلِدُونَ ﴾
[الأعرَاف: 42]
﴿والذين آمنوا وعملوا الصالحات لا نكلف نفسا إلا وسعها أولئك أصحاب الجنة﴾ [الأعرَاف: 42]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo amene akhulupirira ndikumachita zabwino, sitikakamiza munthu aliyense koma chimene angachithe, awo ndiwo anthu a ku Munda wamtendere. M’menemo iwo akakhala nthawi yaitali |