×

Ndithudi Ife tidatumiza Nowa kwa anthu ake ndipo iye adati: “Oh anthu 7:59 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:59) ayat 59 in Chichewa

7:59 Surah Al-A‘raf ayat 59 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 59 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿لَقَدۡ أَرۡسَلۡنَا نُوحًا إِلَىٰ قَوۡمِهِۦ فَقَالَ يَٰقَوۡمِ ٱعۡبُدُواْ ٱللَّهَ مَا لَكُم مِّنۡ إِلَٰهٍ غَيۡرُهُۥٓ إِنِّيٓ أَخَافُ عَلَيۡكُمۡ عَذَابَ يَوۡمٍ عَظِيمٖ ﴾
[الأعرَاف: 59]

Ndithudi Ife tidatumiza Nowa kwa anthu ake ndipo iye adati: “Oh anthu anga! Pembedzani Mulungu! Inu mulibe mulungu wina kupatula Iye yekha. Ndithudi ine ndili kuchita mantha ndi chilango chowawa chimene chidzadza pa inu patsiku lalikulu.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لقد أرسلنا نوحا إلى قومه فقال ياقوم اعبدوا الله ما لكم من, باللغة نيانجا

﴿لقد أرسلنا نوحا إلى قومه فقال ياقوم اعبدوا الله ما لكم من﴾ [الأعرَاف: 59]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithudi, tidamtumiza Nuh kwa anthu ake. (Iye) adati: “E inu anthu anga! Pembedzani Allah. Inu mulibe mulungu wina koma Iye. Ndithu ine ndikukuoperani chilango cha tsiku lalikulu.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek